Sing and Do the Actions

Bilimankhwe Bilimankhwe

Bilimankhwe Bilimankhwe maso anatupa ninjiii?
Kwathu malilo msamaseke ana inuuu kwayera mbeeee mbeee mbeee

Ine mdzachoka pamudzi pano
Mukhalepo nokha pa mudzi pano
Tawonani pa khomo pangapa
Payera mbeeee mbeeee mbeee x2

Chule Chule Iwe

Chule Chule Iwe. Bwantasa. Ndakutuma Madzi. Bwantasa. Wakatenga thope. Bwantasa. Aaaa Iya. Bwantasa

Chule the frog Chule the frog. Webbed toes. I asked for water. Webbed toes. You bring me mud. Webbed toes. Chule the frog Chule the frog. Webbed toes.